Masalimo 44:8 - Buku Lopatulika8 Mwa Mulungu tidzitamanda tsiku lonse, ndipo dzina lanu tidzaliyamika kosatha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Mwa Mulungu tidzitamanda tsiku lonse, ndipo dzina lanu tidzaliyamika kosatha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Takhala tikunyadira mphamvu za Mulungu nthaŵi zonse, ndipo tidzakuthokozani mpaka muyaya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Timanyadira mwa Mulungu wathu tsiku lonse, ndipo tidzatamanda dzina lanu kwamuyaya. Onani mutuwo |