Masalimo 44:25 - Buku Lopatulika25 Pakuti moyo wathu waweramira kufumbi, pamimba pathu pakangamira dziko lapansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Pakuti moyo wathu waweramira kufumbi, pamimba pathu pakangamira dziko lapansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Ife tagwa pansi m'fumbi, thupi lathu langoti thapsa pa dothi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Tatsitsidwa pansi mpaka pa fumbi; matupi athu amatirira pa dothi. Onani mutuwo |