Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 44:23 - Buku Lopatulika

23 Galamukani, mugoneranji, Ambuye? Ukani, musatitaye chitayire.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 Galamukani, mugoneranji, Ambuye? Ukani, musatitaye chitayire.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Dzukani, Inu Ambuye. Chifukwa chiyani mukukhala ngati mwagona? Khalani maso, musatitaye kotheratu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Dzukani Ambuye! Nʼchifukwa chiyani mukugona! Dziwutseni nokha! Musatikane kwamuyaya.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 44:23
11 Mawu Ofanana  

Chifukwa cha kupasuka kwa ozunzika, chifukwa cha kuusa moyo kwa aumphawi, ndiuka tsopano, ati Yehova; ndidzamlonga mosungika muja alakalakamo.


Galamukani, ndipo khalani maso kundiweruzira mlandu wanga, Mulungu wanga ndi Ambuye wanga.


Koma mwatitaya, ndi kutinyazitsa; ndipo simutuluka nao makamu a nkhondo athu.


Ukani Yehova mu mkwiyo wanu, nyamukani chifukwa cha ukali wa akundisautsa; ndipo mugalamukire ine; mwalamulira chiweruzo.


Mulungu, munatitayiranji chitayire? Mkwiyo wanu ufukiranji pa nkhosa za kubusa kwanu?


Kodi Ambuye adzataya nthawi yonse? Osabwerezanso kukondwera nafe.


Pamenepo Ambuye anauka ngati wam'tulo; ngati chiphona chakuchita nthungululu ndi vinyo.


Yehova mutayiranji moyo wanga? Ndi kundibisira nkhope yanu?


Galamuka, galamuka, khala ndi mphamvu, mkono wa Yehova; galamuka monga masiku akale, mibadwo ya nthawi zakale. Kodi si ndiwe amene unadula Rahabu zipinjirizipinjiri; amene unapyoza chinjoka chamnyanja chija?


Ndipo Iye mwini anali kutsigiro, nagona tulo pamtsamiro; ndipo anamuutsa Iye nanena kwa Iye, Mphunzitsi, kodi simusamala kuti titayika ife?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa