Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 44:21 - Buku Lopatulika

21 Mulungu sakadasanthula ichi kodi? Pakuti adziwa zinsinsi za mtima.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 Mulungu sakadasanthula ichi kodi? Pakuti adziwa zinsinsi za mtima.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 kodi Mulungu sakadazipeza zimenezi? Paja Iye amadziŵa zinsinsi zonse zamumtima.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 kodi Mulungu wathu sakanazidziwa zimenezi, pakuti Iye amadziwa zinsinsi zamumtima?

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 44:21
12 Mawu Ofanana  

ndidzatani ponyamuka Mulungu? Ndipo pondizonda Iye ndidzamnyankha chiyani?


Nanga sapenya njira zanga, ndi kuwerenga moponda mwanga monse?


Pakuti Mulungu adzanena mlandu wa zochita zonse, ndi zobisika zonse, ngakhale zabwino ngakhale zoipa.


Ine Yehova ndisanthula mtima, ndiyesa impso, kuti ndimpatse munthu yense monga mwa njira zake, monga zipatso za ntchito zake.


Kodi munthu angathe kubisala mobisika kuti ndisamuone iye? Ati Yehova. Kodi Ine sindidzala kumwamba ndi dziko lapansi? Ati Yehova.


tsiku limene Mulungu adzaweruza ndi Khristu Yesu zinsinsi za anthu, monga mwa Uthenga wanga Wabwino.


Chifukwa chake musaweruze kanthu isanadze nthawi yake, kufikira akadze Ambuye, amenenso adzaonetsera zobisika za mdima, nadzasonyeza zitsimikizo za mtima; ndipo pamenepo yense adzakhala nao uyamiko wake wa kwa Mulungu.


Ndipo ndidzaononga ana ake ndi imfa; ndipo idzazindikira Mipingo yonse kuti Ine ndine Iye amene ayesa impso ndi mitima; ndipo ndidzaninkha kwa yense wa inu monga mwa ntchito zanu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa