Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 44:16 - Buku Lopatulika

16 Chifukwa cha mau a wotonza wochitira mwano; chifukwa cha mdani ndi wobwezera chilango.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Chifukwa cha mau a wotonza wochitira mwano; chifukwa cha mdani ndi wobwezera chilango.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 pakumva mau a anthu onditonza ndi onditukwana, poona mdani wanga ndi munthu wolipsira.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 chifukwa cha mawu otonza a iwo amene amandinyoza ndi kundichita chipongwe, chifukwa cha mdani amene watsimikiza kubwezera.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 44:16
9 Mawu Ofanana  

Ndikakhala woipa, tsoka ine; ndikakhala wolungama, sindidzakweza mutu wanga; ndadzazidwa ndi manyazi, koma penyani kuzunzika kwanga.


Wotsutsanayo adzatonza kufikira liti, Mulungu? Kodi mdani adzanyoza dzina lanu nthawi yonse?


Mukumbukire ichi, Yehova, mdaniyo anatonza, ndipo anthu opusa ananyoza dzina lanu.


Ndipo anansi athu amene anatonza Inu muwabwezere chotonza chao, kasanu ndi kawiri kumtima kwao, Ambuye.


M'kamwa mwa makanda ndi oyamwa munakhazikitsa mphamvu, chifukwa cha otsutsana ndi Inu, kuti muwaletse mdani ndi wobwezera chilango.


Tcherani makutu anu, Yehova, nimumve; tsegulani maso anu, Yehova, nimuone; ndi kumva mau onse a Senakeribu, amene watumiza kumtonza Mulungu wamoyo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa