Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 44:15 - Buku Lopatulika

15 Tsiku lonse chimpepulo changa chikhala pamaso panga, ndipo manyazi a pankhope panga andikuta.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Tsiku lonse chimpepulo changa chikhala pamaso panga, ndipo manyazi a pankhope panga andikuta.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Tsiku lonse ndimangodziwona kuti ndine munthu wopandapake. Nkhope yanga yagwa chifukwa cha manyazi,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Manyazi anga ali pamaso panga tsiku lonse ndipo nkhope yanga yaphimbidwa ndi manyazi

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 44:15
11 Mawu Ofanana  

pamenepo Ine ndidzalikha Aisraele kuwachotsera m'dziko ndidawapatsali; ndipo nyumba ino ndapatulira dzina langayi ndidzaitaya kosapenyeka; ndipo Israele adzakhala ngati mwambi ndi nkhani pakati pa anthu onse.


Ndipo Yehova anatuma wamthenga amene anaononga ngwazi zamphamvu zonse, ndi atsogoleri, ndi akazembe, kuchigono cha mfumu ya Asiriya. Nabwerera iye ndi nkhope yamanyazi kudziko lake. Ndipo atalowa m'nyumba ya mulungu wake, iwo otuluka m'matumbo mwake anamupha ndi lupanga pomwepo.


ndipo ndinati, Mulungu wanga, ndigwa nkhope, ndi kuchita manyazi kuweramutsa nkhope yanga kwa inu Mulungu wanga, popeza mphulupulu zathu zachuluka pamutu pathu, ndi kupalamula kwathu kwakula kufikira mu Mwamba.


Anandiyesanso chitonzo cha anthu; ndipo ndakhala ngati munthu womthira malovu pankhope pake.


Pakuti ndalola chotonza chifukwa cha Inu, chimpepulo chakuta nkhope yanga.


Adani a moyo wanga achite manyazi, nathawe; chotonza ndi chimpepulo zikute ondifunira choipa.


Munafupikitsa masiku a mnyamata wake; munamkuta nao manyazi.


Tigone m'manyazi athu, kunyala kwathu kutifunde ife; pakuti tamchimwira Yehova Mulungu wathu, ife ndi makolo athu, kuyambira ubwana wathu kufikira lero lomwe; ndipo sitidamvere mau a Yehova Mulungu wathu.


Tili ndi manyazi, chifukwa tamva mnyozo; manyazi aphimba nkhope zathu; pakuti alendo alowa m'malo opatulika a nyumba ya Yehova.


Onse opita panjira akuombera manja: Atsonya, napukusira mitu yao pa mwana wamkazi wa Yerusalemu, nati, kodi uwu ndi mzinda wotchedwa wokongola, wangwiro, wokondweretsa dziko lonse?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa