Masalimo 44:13 - Buku Lopatulika13 Mutisandutsa chotonza kwa anzathu, ndi choseketsa ndi cholalatitsa iwo akutizinga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Mutisandutsa chotonza kwa anzathu, ndi choseketsa ndi cholalatitsa iwo akutizinga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Inu mwatisandutsa anthu onyozeka kwa anzathu oyandikana nafe, anthu otizungulira amatiseka ndi kutinyodola. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Mwachititsa kuti tikhale chochititsa manyazi kwa anthu a mitundu ina, chonyozeka ndi chothetsa nzeru kwa iwo amene atizungulira. Onani mutuwo |