Masalimo 40:15 - Buku Lopatulika15 Apululuke, mobwezera manyazi ao amene anena nane, Hede, hede. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Apululuke, mobwezera manyazi ao amene anena nane, Hede, hede. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Amene amandinyodola kuti, “Ha, Ha,” achoke ndi kuchita manyazi poona kuti alephera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Iwo amene amanena kwa ine kuti, “Hee! Hee!” abwerere akuchita manyazi. Onani mutuwo |