Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 37:30 - Buku Lopatulika

30 Pakamwa pa wolungama palankhula zanzeru, ndi lilime lake linena chiweruzo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

30 Pakamwa pa wolungama palankhula zanzeru, ndi lilime lake linena chiweruzo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

30 Munthu wabwino amalankhula zanzeru, pakamwa pake pamatuluka zachilungamo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

30 Pakamwa pa munthu wolungama pamayankhula za nzeru, ndipo lilime lake limayankhula zolungama.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 37:30
12 Mawu Ofanana  

Pakamwa panga padzafotokozera chilungamo chanu, ndi chipulumutso chanu tsiku lonse; pakuti sindidziwa mawerengedwe ake.


Lilime langa lomwe lidzalankhula za chilungamo chanu tsiku lonse, pakuti ofuna kundichitira choipa achita manyazi, nadodoma.


Lilime la wolungama likunga siliva wosankhika; koma mtima wa oipa uli wachabe.


Milomo ya wolungama imadyetsa ambiri; koma zitsiru zimafa posowa nzeru.


M'kamwa mwa wolungama mulankhula nzeru; koma lilime lokhota lidzadulidwa.


Milomo ya anzeru iwanditsa nzeru, koma mtima wa opusa suli wolungama.


Mafuta ndi zonunkhira zikondweretsa mtima, ndi ubwino wa bwenzi uteronso pakupangira uphungu.


Munthu wabwino atulutsa zabwino m'chuma chake chabwino, ndi munthu woipa atulutsa zoipa m'chuma chake choipa.


Nkhani yonse yovunda isatuluke m'kamwa mwanu, koma ngati pali ina yabwino kukumangirira monga mofunika ndiyo, kuti ipatse chisomo kwa iwo akumva.


Mau anu akhale m'chisomo, okoleretsa, kuti mukadziwe inu mayankhidwe anu a kwa yense akatani.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa