Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 37:26 - Buku Lopatulika

26 Tsiku lonse achitira chifundo, nakongoletsa; ndipo mbumba zake zidalitsidwa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

26 Tsiku lonse achitira chifundo, nakongoletsa; ndipo mbumba zake zidalitsidwa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

26 Nthaŵi zonse munthu wolungama amapatsa mosaumira, ndipo amakongoza mwaufulu, ana ake amakhala madalitso.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

26 Iwo ndi owolowamanja nthawi zonse ndipo amabwereketsa mwaufulu; ana awo adzadalitsika.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 37:26
10 Mawu Ofanana  

Wodala munthu wakuchitira chifundo, nakongoletsa; adzalimbika nao mlandu wake poweruzidwa.


Anagawagawa, anapatsa aumphawi; chilungamo chake chikhalitsa kosatha; nyanga yake idzakwezeka ndi ulemu.


Popeza analimbitsa mipiringidzo ya zitseko zanu: Anadalitsa ana anu m'kati mwanu.


Woipa akongola, wosabweza, koma wolungama achitira chifundo, napereka.


Wolungama woyenda mwangwiro, anake adala pambuyo pake.


Ena asirira modukidwa tsiku lonse; koma wolungama amapatsa osamana.


ndipo ndidzawapatsa mtima umodzi ndi njira imodzi, kuti andiope Ine masiku onse; kuwachitira zabwino, ndi ana ao pambuyo pao;


Odala ali akuchitira chifundo; chifukwa adzalandira chifundo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa