Masalimo 37:22 - Buku Lopatulika22 Pakuti iwo amene awadalitsa adzalandira dziko lapansi; koma iwo amene awatemberera adzadulidwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Pakuti iwo amene awadalitsa adzalandira dziko lapansi; koma iwo amene awatemberera adzadulidwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Anthu amene Chauta adaŵadalitsa, adzalandira dziko kuti likhale lao, koma amene Chauta adaŵatemberera adzaonongeka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Iwo amene Yehova amawadalitsa adzalandira dziko, koma amene Iye amawatemberera adzachotsedwa. Onani mutuwo |