Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 37:21 - Buku Lopatulika

21 Woipa akongola, wosabweza, koma wolungama achitira chifundo, napereka.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 Woipa akongola, wosabweza, koma wolungama achitira chifundo, napereka.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Munthu woipa amakonda ngongole koma satha kubweza, koma munthu wabwino ali ndi mtima wokoma ndi wopatsa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Oyipa amabwereka ndipo sabweza koma olungama amapereka mowolowamanja.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 37:21
18 Mawu Ofanana  

Wodala munthu wakuchitira chifundo, nakongoletsa; adzalimbika nao mlandu wake poweruzidwa.


Anagawagawa, anapatsa aumphawi; chilungamo chake chikhalitsa kosatha; nyanga yake idzakwezeka ndi ulemu.


Wolemera alamulira osauka; ndipo wokongola ndiye kapolo wa womkongoletsa.


Koma mfulu aganizira zaufulu, nakhazikika m'zaufulu zomwe.


Munthu aliyense akakupempha kanthu, umpatse; ndi iye amene alanda zako, usazipemphanso.


Ndipo ophunzira, yense monga anakhoza, anatsimikiza mtima kutumiza zothandiza abale akukhala mu Yudeya;


M'zinthu zonse ndinakupatsani chitsanzo, chakuti pogwiritsa ntchito, kotero muyenera kuthandiza ofooka ndi kukumbuka mau a Ambuye Yesu, kuti anati yekha, Kupatsa kutidalitsa koposa kulandira.


Pakuti mudziwa chisomo cha Ambuye wathu Yesu Khristu, kuti, chifukwa cha inu anakhala wosauka, angakhale anali wolemera, kuti inu ndi kusauka kwake mukakhale olemera.


Yehova adzakutsegulirani chuma chake chokoma, ndicho thambo la kumwamba, kupatsa dziko lanu mvula m'nyengo yake, ndi kudalitsa ntchito zonse za dzanja lanu; ndipo mudzakongoletsa amitundu ambiri, osakongola nokha.


Koma musaiwale kuchitira chokoma ndi kugawira ena; pakuti nsembe zotere Mulungu akondwera nazo.


pakuti Mulungu sali wosalungama kuti adzaiwala ntchito yanu, ndi chikondicho mudachionetsera kudzina lake, umo mudatumikira oyera mtima ndi kuwatumikirabe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa