Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 37:19 - Buku Lopatulika

19 Sadzachita manyazi m'nyengo yoipa, ndipo m'masiku a njala adzakhuta.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

19 Sadzachita manyazi m'nyengo yoipa, ndipo m'masiku a njala adzakhuta.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

19 Pa nthaŵi ya mavuto sadzazunzika, pa nthaŵi yanjala, adzakhala nazo zakudya zochuluka.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

19 Pa nthawi ya mavuto iwo sadzafota; mʼmasiku a njala adzakhala ndi zinthu zambiri.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 37:19
8 Mawu Ofanana  

Kupulumutsa moyo wao kwa imfa, ndi kuwasunga ndi moyo m'nyengo ya njala.


Yehova samvetsa njala moyo wa wolungama; koma amainga chifuniro cha wochimwa.


Pakuti munthu sadziwatu mphindi yake; monga nsomba zigwidwa mu ukonde woipa, ndi mbalame zikodwa mumsampha, momwemo ana a anthu amagwidwa ndi nthawi ya tsoka, ngati msampha umene uwagwera modzidzimuka.


iye adzakhala pamsanje; malo ake ochinjikiza adzakhala malinga amiyala; chakudya chake chidzapatsidwa kwa iye; madzi ake adzakhala chikhalire.


Chifukwa chake wochenjerayo akhala chete nthawi yomweyo; pakuti ndiyo nthawi yoipa.


Chifukwa chake atero Yehova, Taonani, ndilingirira choipa pa banja ili, chimene simudzachotsako makosi anu, kapena kuyenda modzikuza inu; pakuti nyengo iyi ndi yoipa.


akuchita machawi, popeza masiku ali oipa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa