Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 37:16 - Buku Lopatulika

16 Zochepa zake za wolungama zikoma koposa kuchuluka kwao kwa oipa ambiri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Zochepa zake za wolungama zikoma koposa kuchuluka kwao kwa oipa ambiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Nkwabwino kukhala m'chilungamo ndi kusauka, kupambana kukhala nazo zokoma zambiri zimene munthu woipa ali nazo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Zabwino zochepa zimene olungama ali nazo ziposa chuma cha anthu oyipa ambiri;

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 37:16
9 Mawu Ofanana  

Wolungama adya nakhutitsa moyo wake; koma mimba ya oipa idzasowa.


Zapang'ono, pokhala chilungamo, ziposa phindu lalikulu lopanda chiweruzo.


Yehova atemberera za m'nyumba ya woipa; koma adalitsa mokhalamo olungama.


ndingakhute ndi kukukanani, ndi kuti, Yehova ndani? Kapena ndingasauke ndi kuba, ndi kutchula dzina la Mulungu wanga pachabe.


Pakuti yemwe Mulungu amuyesa wabwino ampatsa nzeru ndi chidziwitso ndi chimwemwe; koma wochimwa amlawitsa vuto la kusonkhanitsa ndi kukundika, kuti aperekere yemwe Mulungu amuyesa wabwino. Ichinso ndi chabe ndi kungosautsa mtima.


Dzanja limodzi lodzala pali mtendere liposa manja awiri oti thoo pali vuto ndi kungosautsa mtima.


Mutipatse ife lero chakudya chathu chalero.


Koma chipembedzo pamodzi ndi kudekha chipindulitsa kwakukulu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa