Masalimo 37:14 - Buku Lopatulika14 Oipa anasolola lupanga, nakoka uta wao; alikhe ozunzika ndi aumphawi, aphe amene ali oongoka m'njira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Oipa anasolola lupanga, nakoka uta wao; alikhe ozunzika ndi aumphawi, aphe amene ali oongoka m'njira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Anthu oipa amasolola lupanga, ndipo amakoka mauta, kuti aphe anthu ovutika ndi osoŵa, amene amayenda molungama. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Oyipa amasolola lupanga ndi kupinda uta kugwetsa osauka ndi osowa, kupha iwo amene njira zawo ndi zolungama. Onani mutuwo |