Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 37:13 - Buku Lopatulika

13 Ambuye adzamseka, popeza apenya kuti tsiku lake likudza.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Ambuye adzamseka, popeza apenya kuti tsiku lake likudza.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Koma Chauta amamseka munthu woipayo, poti amaona kuti tsiku lake la kuwonongeka likubwera.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 koma Ambuye amaseka oyipa pakuti Iye amadziwa kuti tsiku lawo likubwera.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 37:13
9 Mawu Ofanana  

Akudza m'mbuyo adzadabwa nalo tsiku lake, monga aja omtsogolera anagwidwa mantha.


Wokhala m'mwambayo adzaseka; Ambuye adzawanyoza.


Inetu ndidzachitira chiphwete tsoka lanu, ndidzatonyola pakudza mantha anu;


Chifukwa padzakhala tsiku la Yehova wa makamu pa zonse zonyada ndi zakudzikuza, ndi pa zonse zotukulidwa; ndipo zidzatsitsidwa;


Iphani ng'ombe zamphongo zake zonse; zitsikire kukaphedwa; tsoka iwo! Pakuti tsiku lao lafika, tsiku la kulanga kwao.


Ndipo iwe wolasidwa woipa, kalonga wa Israele, amene lafika tsiku lako, nthawi ya mphulupulu yotsiriza;


Akuonera zopanda pake, akuombezera mabodza, lupanga likugoneka pa makosi a oipa olasidwa, amene lafika tsiku lao nthawi ya mphulupulu yotsiriza.


Kumasulira kwake kwa mau awa ndi uku: MENE, Mulungu anawerenga ufumu wanu, nautha.


Nati Davide, Pali Yehova, Yehova adzamkantha iye; kapena tsiku la imfa yake lidzafika; kapena adzatsikira kunkhondo, nadzafako.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa