Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 36:11 - Buku Lopatulika

11 Phazi la akudzikuza lisandifikire ine, ndi dzanja la oipa lisandichotse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Phazi la akudzikuza lisandifikire ine, ndi dzanja la oipa lisandichotse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Musalole kuti mapazi a anthu odzikuza andipondereze, ndipo kuti manja a anthu oipa andipirikitse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Musalole kuti phazi la wodzikuza libwere kulimbana nane, kapena dzanja la oyipa kundithamangitsa.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 36:11
16 Mawu Ofanana  

Podzikuza woipa apsereza waumphawi; agwe m'chiwembu anapanganacho.


Mumkhalire chikole mtumiki wanu chimkomere; odzikuza asandisautse.


Odzikuza anandinyoza kwambiri: koma sindinapatukanso nacho chilamulo chanu.


Odzikuza anandipangira bodza: Ndidzasunga malangizo anu ndi mtima wanga wonse.


Odzikuza anandikumbira mbuna, ndiwo osasamalira chilamulo chanu.


Ndaika Yehova patsogolo panga nthawi zonse; popeza ali padzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka.


Iye yekhayo ndiye thanthwe langa ndi chipulumutso changa, msanje wanga, sindidzagwedezeka.


Ndidzachiika m'dzanja la iwo amene avutitsa iwe; amene anena kumoyo wako, Gwada pansi kuti ife tipite; ndipo iwe wagonetsa pamsana pako monga pansi, ndi monga khwalala kwa iwo amene apita pamenepo.


Tsono ine Nebukadinezara ndiyamika, ndi kukuza, ndi kulemekeza Mfumu ya Kumwamba, pakuti ntchito zake zonse nzoona, ndi njira zake chiweruzo; ndi oyenda m'kudzikuza kwao, Iye akhoza kuwachepetsa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa