Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 36:10 - Buku Lopatulika

10 Tanimphitsani chifundo chanu pa iwo akudziwa Inu; ndi chilungamo chanu pa oongoka mtima.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Tanimphitsani chifundo chanu pa iwo akudziwa Inu; ndi chilungamo chanu pa oongoka mtima.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Musaleke kuŵakonda ndi chikondi chanu chosasinthika anthu okudziŵani, pitirizani kuŵachitira zokoma anthu olungama mtima.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Pitirizani chikondi chanu pa iwo amene amakudziwani, chilungamo chanu kwa olungama mtima.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 36:10
17 Mawu Ofanana  

Koma chifundo cha Yehova ndicho choyambira nthawi yosayamba kufikira nthawi yosatha kwa iwo akumuopa Iye, ndi chilungamo chake kufikira kwa ana a ana;


ndipo iwo akudziwa dzina lanu adzakhulupirira Inu; pakuti, Inu Yehova, simunawasiye iwo akufuna Inu.


Inu a nyumba ya Yakobo, tiyeni, tiyende m'kuwala kwa Yehova.


Iye anaweruza mlandu wa aumphawi ndi osowa; kumeneko kunali kwabwino. Kodi kumeneko si kundidziwa Ine? Ati Yehova.


Ndipo ndidzapatsa iwo mtima wakundidziwa, kuti ndine Yehova, nadzakhala anthu anga, ndipo Ine ndidzakhala Mulungu wao; pakuti adzabwera kwa Ine ndi mtima wao.


Yehova anaonekera kwa ine kale, ndi kuti, Inde, ndakukonda iwe ndi chikondi chosatha; chifukwa chake ndakukoka iwe ndi kukukomera mtima.


Koma moyo wosatha ndi uwu, kuti akadziwe Inu Mulungu woona yekha, ndi Yesu Khristu amene munamtuma.


Ndipo sadzaphunzitsa yense mfulu mnzake, ndipo yense mbale wake, ndi kuti, Zindikira Ambuye: Pakuti onse adzadziwa Ine, kuyambira wamng'ono kufikira wamkulu wa iwo.


amene musungidwa ndi mphamvu ya Mulungu mwa chikhulupiriro, kufikira chipulumutso chokonzeka kukavumbulutsidwa nthawi yotsiriza.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa