Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 35:2 - Buku Lopatulika

2 Gwirani chikopa chotchinjiriza, ukani kundithandiza.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Gwirani chikopa chotchinjiriza, ukani kundithandiza.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Gwirani chishango ndi lihawo, ndipo fulumirani mundithandize.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Tengani chishango ndi lihawo; dzukani ndipo bwerani mundithandize.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 35:2
6 Mawu Ofanana  

Adzakufungatira ndi nthenga zake, ndipo udzathawira kunsi kwa mapiko ake; choonadi chake ndicho chikopa chotchinjiriza.


Yehova ndiye wankhondo; dzina lake ndiye Yehova.


Achokera m'dziko lakutali, kumalekezero a thambo, ngakhale Yehova, ndi zida za mkwiyo wake, kuti aononge dziko lonse.


Yehova adzatuluka ngati munthu wamphamvu; adzautsa nsanje ngati munthu wa nkhondo; Iye adzafuula, inde adzakuwa zolimba; adzachita zamphamvu pa adani ake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa