Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 34:22 - Buku Lopatulika

22 Yehova aombola moyo wa anyamata ake, ndipo sadzawatsutsa kumlandu onse akukhulupirira Iye.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Yehova aombola moyo wa anyamata ake, ndipo sadzawatsutsa kumlandu onse akukhulupirira Iye.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Chauta amaombola moyo wa atumiki ake. Palibe wothaŵira kwa Iye amene adzalangidwe.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Yehova amawombola atumiki ake; aliyense amene amathawira kwa Iye sadzapezeka wolakwa.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 34:22
17 Mawu Ofanana  

mthenga amene anandiombola ine ku zoipa zonse, adalitse anyamatawa; dzina langa litchulidwe pa iwo, ndi dzina la makolo anga Abrahamu ndi Isaki; iwo akule, nakhale khamu pakati padziko lapansi.


Ndipo Davide anayankha Rekabu ndi Baana mbale wake, ana a Rimoni wa ku Beeroti, nanena nao, Pali Yehova amene anaombola moyo wanga m'masautso onse,


Ndipo mfumu inalumbira, niti, Pali Yehova amene anapulumutsa moyo wanga m'nsautso monse,


amene aombola moyo wako ungaonongeke; nakuveka korona wa chifundo ndi nsoni zokoma:


Ndipo adzaombola Israele ku mphulupulu zake zonse.


Ndipereka mzimu wanga m'dzanja lanu; mwandiombola, Inu Yehova, Mulungu wa choonadi.


Woipa apangira chiwembu wolungama, namkukutira mano.


Lupanga lao lidzalowa m'mtima mwao momwe, ndipo mauta ao adzathyoledwa.


Milomo yanga idzafuula mokondwera poimbira Inu nyimbo; inde, moyo wanga umene munaombola.


Ambuye munanenera moyo wanga milandu yake; munaombola moyo wanga.


amene musungidwa ndi mphamvu ya Mulungu mwa chikhulupiriro, kufikira chipulumutso chokonzeka kukavumbulutsidwa nthawi yotsiriza.


Ndipo aimba nyimbo yatsopano, ndi kunena, Muyenera kulandira bukulo, ndi kumasula zizindikiro zake; chifukwa mwaphedwa, ndipo mwagulira Mulungu ndi mwazi wanu anthu a mafuko onse, ndi manenedwe onse, ndi mitundu yonse,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa