Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 33:13 - Buku Lopatulika

13 Yehova apenyerera m'mwamba; aona ana onse a anthu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Yehova apenyerera m'mwamba; aona ana onse a anthu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Chauta ali kumwamba, amayang'ana pansi ndi kuwona anthu onse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Kuchokera kumwamba Yehova amayangʼana pansi ndi kuona anthu onse;

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 33:13
13 Mawu Ofanana  

Ndipo Mulungu anaona dziko lapansi, ndipo taonani, linavunda; pakuti anthu onse anavunditsa njira yao padziko lapansi.


Pakuti maso a Yehova ayang'ana uko ndi uko m'dziko lonse lapansi, kudzionetsera wamphamvu kwa iwo amene mtima wao uli wangwiro ndi Iye. Mwachita chopusa m'menemo; pakuti kuyambira tsopano mudzaona nkhondo.


Pakuti adziwa anthu opanda pake, napenyanso mphulupulu, ngakhale saisamalira.


Pakuti apenyerera malekezero a dziko lapansi, naona pansi pa thambo ponse;


Pakuti anapenya pansi ali kumwamba kuli malo ake opatulika; Yehova pokhala kumwamba anapenya dziko lapansi;


Yehova ali mu Kachisi wake woyera, Yehova, mpando wachifumu wake uli mu Mwamba; apenyerera ndi maso ake, ayesa ana a anthu ndi zikope zake.


Yehova mu Mwamba anaweramira pa ana a anthu, kuti aone ngati aliko wanzeru, wakufuna Mulungu.


Mulungu m'mwamba anaweramira pa ana a anthu, kuti aone ngati aliko wanzeru, wakufuna Mulungu.


Achita ufumu mwa mphamvu yake kosatha; maso ake ayang'anira amitundu; opikisana ndi Iye asadzikuze.


Maso a Yehova ali ponseponse, nayang'anira oipa ndi abwino.


kufikira Yehova adzazolika kumwamba ndi kuona.


Ndipo palibe cholembedwa chosaonekera pamaso pake, koma zonse zikhala za pambalambanda ndi zovundukuka pamaso pake pa Iye amene tichita naye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa