Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 31:9 - Buku Lopatulika

9 Mundichitire chifundo, Yehova, pakuti ndasautsika ine. Diso langa, mzimu wanga, ndi mimba yanga, zapuwala ndi mavuto.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Mundichitire chifundo, Yehova, pakuti ndasautsika ine. Diso langa, mzimu wanga, ndi mimba yanga, zapuwala ndi mavuto.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Tsono mundikomere mtima, Inu Chauta, pakuti ndili m'zovuta. Maso anga atupa chifukwa cha chisoni. Mumtima mwanga ndi m'thupi momwe mwadzaza zovuta.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Mundichitire chifundo Inu Yehova pakuti ndili pa mavuto; maso anga akulefuka ndi chisoni, mʼmoyo mwanga ndi mʼthupi mwanga momwe mukupweteka.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 31:9
19 Mawu Ofanana  

Iye ananditulutsanso ku malo aakulu; Iye anandipulumutsa, chifukwa akondwera ndi ine.


M'diso mwanga muchita chizirezire chifukwa cha chisoni, ndi ziwalo zanga zonse zilibe chithunzi.


Iwo akukhala mumdima ndi mu mthunzi wa imfa, omangika ndi kuzunzika ndi chitsulo;


Yehova anandibwezera monga mwa chilungamo changa; anandisudzula monga mwa kusisira kwa manja anga.


Ndidzalondola adani anga, ndi kuwapeza, ndipo sindidzabwerera asanathe psiti.


Pakuti moyo wathu waweramira kufumbi, pamimba pathu pakangamira dziko lapansi.


Lapuwala diso langa chifukwa cha chisoni; lakalamba chifukwa cha onse akundisautsa.


zimene inazitchula milomo yanga, ndinazinena pakamwa panga posautsika ine.


Popeza andisautsa tsiku lonse, nandilanga mamawa monse,


Likatha thupi langa ndi mtima wanga, Mulungu ndiye thanthwe la mtima wanga, ndi cholandira changa chosatha.


Diso langa lapuwala chifukwa cha kuzunzika kwanga: Ndimaitana Inu, Yehova, tsiku lonse; nditambalitsira manja anga kwa Inu.


Maso athu athedwa, tikali ndi moyo, poyembekeza thandizo chabe; kudikira tinadikira mtundu wosatha kupulumutsa.


Chifukwa cha ichi mtima wathu ufooka, chifukwa cha izi maso athu achita chimbuuzi;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa