Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 31:16 - Buku Lopatulika

16 Walitsani nkhope yanu pa mtumiki wanu, mundipulumutse ndi chifundo chanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Walitsani nkhope yanu pa mtumiki wanu, mundipulumutse ndi chifundo chanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Yang'aneni mtumiki wanune mwa kukoma mtima kwanu, pulumutseni chifukwa cha chikondi chanu chosasinthika.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Walitsani nkhope yanu pa mtumiki wanu; pulumutseni mwa chikondi chanu chosatha.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 31:16
17 Mawu Ofanana  

Ndipo anawakumbukira chipangano chake, naleza monga mwa kuchuluka kwa chifundo chake.


Chipulumutso ncha Yehova; dalitso lanu likhale pa anthu anu.


Inu, Yehova, munakhazikitsa phiri langa ndi kuyanja kwanu; munabisa nkhope yanu; ndinaopa.


Ambiri amati, Adzationetsa chabwino ndani? Weramutsirani ife kuunika kwa nkhope yanu, Yehova.


Mundichitire ine chifundo, Mulungu, monga mwa kukoma mtima kwanu; monga mwa unyinji wa nsoni zanu zokoma mufafanize machimo anga.


Bwererani Yehova, landitsani moyo wanga; ndipulumutseni chifukwa cha kukoma mtima kwanu.


Atichitire chifundo Mulungu, ndi kutidalitsa, atiwalitsire nkhope yake;


Mutibweze, Yehova Mulungu wa makamu; nimuwalitse nkhope yanu, ndipo tidzapulumuka.


Mutibweze, Mulungu; nimuwalitse nkhope yanu, ndipo tidzapulumuka.


Mulungu wa makamu, mutibweze; nimuwalitse nkhope yanu, ndipo tidzapulumuka.


Ambuye Mulungu wathu ndiye wachifundo, ndi wokhululukira; pakuti tampandukira Iye;


Pakuti anati ndi Mose, Ndidzachitira chifundo amene ndimchitira chifundo, ndipo ndidzakhala ndi chisoni kwa iye amene ndikhala naye chisoni.


Ndi kuti Iye akadziwitse ulemerero wake waukulu pa zotengera zachifundo, zimene Iye anazikonzeratu kuulemerero,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa