Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 31:12 - Buku Lopatulika

12 Ndaiwalika m'mtima monga wakufa, ndikhala monga chotengera chosweka.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Ndaiwalika m'mtima monga wakufa, ndikhala monga chotengera chosweka.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Andiiŵala kotheratu ngati munthu wakufa. Ndasanduka ngati chiŵiya chosweka.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Ine ndinayiwalika kwa iwo ngati kuti ndinamwalira; ndakhala ngati mʼphika wosweka.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 31:12
11 Mawu Ofanana  

Iye anandichotsera abale anga kutali, ndi odziwana nane andiyesa mlendo konse.


Anansi anga andisowa, ndi odziwana nane bwino andiiwala.


Popeza ndakhala ngati thumba lofukirira; koma sindiiwala malemba anu.


Udzawathyola ndi ndodo yachitsulo; udzawaphwanya monga mbiya ya woumba.


Ndipo anditchera misampha iwo akufuna moyo wanga; ndipo iwo akuyesa kundichitira choipa alankhula zoononga, nalingirira zonyenga tsiku lonse.


Wodalitsika Yehova kunthawi yonse. Amen ndi Amen.


Ndipo Iye adzagumulapo, monga mbiya ya woumba isweka, ndi kuiswaiswa osaileka; ndipo sipadzapezedwa m'zigamphu zake phale lopalira moto pachoso, ngakhale lotungira madzi padziwe.


ndipo adzawalamulira ndi ndodo yachitsulo, monga zotengera za woumba mbiya ziphwanyika mapale; monga Inenso ndalandira kwa Atate wanga;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa