Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 31:10 - Buku Lopatulika

10 Pakuti moyo wanga watha ndi chisoni, ndi zaka zanga zatha ndi kuusa moyo. Mphamvu yanga yafooka chifukwa cha kusakaza kwanga, ndi mafupa anga apuwala.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Pakuti moyo wanga watha ndi chisoni, ndi zaka zanga zatha ndi kuusa moyo. Mphamvu yanga yafooka chifukwa cha kusakaza kwanga, ndi mafupa anga apuwala.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Moyo wanga ukutha chifukwa cha chisoni, zaka zanganso zikutha chifukwa cha kulira kwambiri. Mphamvu zanga zatheratu chifukwa cha kulakwa kwanga, mafupa anga agooka.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Moyo wanga ukunyeka chifukwa cha kuwawidwa mtima ndi zaka zanga chifukwa cha kubuwula; mphamvu zanga zatha chifuwa cha masautso, ndipo mafupa anga akulefuka.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 31:10
12 Mawu Ofanana  

Pakuti ndikati ndidye, kumadza kuusa moyo kwanga; ndi kudzuma kwanga kumathiridwa ngati madzi.


Ndidzachita uphungu m'moyo mwanga kufikira liti, pokhala ndi chisoni m'mtima mwanga tsiku lonse? Adzandiukira ine mdani wanga kufikira liti?


Imvani, Yehova, liu langa pofuula ine; mundichitirenso chifundo ndipo mundivomereze.


Mumnofu mwanga mulibe chamoyo chifukwa cha ukali wanu; ndipo m'mafupa anga simuzizira, chifukwa cha cholakwa changa.


Pamene mulanga munthu ndi zomdzudzula chifukwa cha mphulupulu, mukanganula kukongola kwake monga mumachita ndi njenjete. Indedi, munthu aliyense ali chabe.


Chokani kwa ine, nonsenu akuchita zopanda pake; pakuti wamva Yehova mau a kulira kwanga.


Musanditaye mu ukalamba wanga; musandisiye, pakutha mphamvu yanga.


Potero anathera masiku ao ndi zopanda pake, ndi zaka zao mwa mantha.


Wozunzika ine ndi wofuna kufa kuyambira ubwana wanga; posenza zoopsa zanu, ndithedwa nzeru.


kuti ndagwidwa ndi chisoni chachikulu ndi kuphwetekwa mtima kosaleka.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa