Masalimo 29:6 - Buku Lopatulika6 Aitumphitsa monga mwanawang'ombe; Lebanoni ndi Sirioni monga msona wa njati. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Aitumphitsa monga mwanawang'ombe; Lebanoni ndi Sirioni monga msona wa njati. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Amagwedeza phiri la Lebanoni kuti lizivinavina ngati likonyani, amavinitsa phiri la Sirioni ngati mwanawanjati. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Iye amachititsa Lebanoni kulumphalumpha ngati mwana wangʼombe, Siriyoni ngati mwana wa njati: Onani mutuwo |