Masalimo 29:5 - Buku Lopatulika5 Liu la Yehova lithyola mitengo yamkungudza; inde Yehova athyola mikungudza ya ku Lebanoni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Liu la Yehova lithyola mitengo yamkungudza; inde Yehova athyola mikungudza ya ku Lebanoni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Liwu la Chauta limathyola mikungudza, Chauta amathyolathyoladi mikungudza ya ku Lebanoni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Liwu la Yehova limathyola mikungudza; Yehova amathyolathyola mikungudza ya ku Lebanoni. Onani mutuwo |