Masalimo 25:8 - Buku Lopatulika8 Yehova ndiye wabwino ndi wolunjika mtima, chifukwa chake adzaphunzitsa olakwa za njira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Yehova ndiye wabwino ndi wolunjika mtima, chifukwa chake adzaphunzitsa olakwa za njira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Chauta ndi wabwino ndi wolungama. Nchifukwa chake amaphunzitsa ochimwa njira zake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Yehova ndi wabwino ndi wolungama; choncho Iye akulangiza ochimwa mʼnjira yake. Onani mutuwo |