Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 25:21 - Buku Lopatulika

21 Ungwiro ndi kuongoka mtima zindisunge, pakuti ndayembekezera Inu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 Ungwiro ndi kuongoka mtima zindisunge, pakuti ndayembekezera Inu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Kukhulupirika kwanga ndi kulungama kwanga kunditeteze, popeza kuti ndakukhulupirirani.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Kukhulupirika ndi kulungama kwanga kunditeteze, chifukwa chiyembekezo changa chili mwa Inu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 25:21
12 Mawu Ofanana  

Mundiweruze, Yehova, pakuti ndayenda mu ungwiro wanga, ndipo ndakhulupirira Yehova, sindadzaterereka.


Koma ine, ndidzayenda mu ungwiro wanga; mundiombole, ndipo ndichitireni chifundo.


Ndipo ine, mundigwirizize mu ungwiro wanga, ndipo mundiike pankhope panu kunthawi yamuyaya.


Yehova aweruza anthu mlandu; mundiweruze, Yehova, monga mwa chilungamo changa, ndi ungwiro wanga uli mwa ine.


Kuongoka mtima kwa olungama kuwatsogolera; koma kukhota kwa achiwembu kudzawaononga.


Wolungama woyenda mwangwiro, anake adala pambuyo pake.


Mulungu wanga watuma mthenga wake, natseka pakamwa pa mikango; ndipo siinandipweteka, chifukwa anandiona wosachimwa pamaso pake, pamaso panunso, mfumu, sindinalakwe.


M'menemonso ndidziyesera ndekha ndikhale nacho nthawi zonse chikumbumtima chosanditsutsa cha kwa Mulungu ndi kwa anthu.


Ndipo Yehova adzabwezera munthu yense chilungamo chake ndi chikhulupiriko chake, popeza Yehova anakuperekani lero m'dzanja langa, koma sindinalole kutukulira dzanja langa pa wodzozedwa wa Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa