Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 25:18 - Buku Lopatulika

18 Penyani mazunzo anga ndi zovuta zanga; ndipo khululukirani zolakwa zanga zonse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Penyani mazunzo anga ndi zovuta zanga; ndipo khululukirani zolakwa zanga zonse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Penyani mazunzo anga ndi mavuto anga, ndipo mundikhululukire machimo anga onse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Penyani mazunzo anga ndi zovuta zanga ndipo mufafanize machimo anga onse.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 25:18
11 Mawu Ofanana  

Kapena Yehova adzayang'anira chosayenerachi alikundichitira ine, ndipo Yehova adzandibwezera chabwino m'malo mwa kunditukwana kwa lero.


Munditembenukire, ndi kundichitira chifundo, monga mumatero nao akukonda dzina lanu.


Penyani kuzunzika kwanga, nimundilanditse; pakuti sindiiwala chilamulo chanu.


Yehova, kumbukirani Davide kuzunzika kwake konse.


Udyo wake unali m'nsalu zake; sunakumbukire chitsiriziro chake; chifukwa chake watsika mozizwitsa; ulibe wakuutonthoza; taonani, Yehova, msauko wanga, pakuti mdaniyo wadzikuza yekha.


Yehova, kumbukirani chotigwerachi, penyani nimuone chitonzo chathu.


Ndipo onani, anabwera naye kwa Iye munthu wamanjenje, wakugona pamphasa: ndipo Yesu pakuona chikhulupiriro chao, anati kwa wodwalayo, Limba mtima, mwana, machimo ako akhululukidwa.


Ambuye wandichitira chotero m'masiku omwe Iye anandipenyera, kuchotsa manyazi anga pakati pa anthu.


nalonjeza chowinda, nati, Yehova wa makamu, mukapenyera ndithu kusauka kwa mdzakazi wanu, ndi kukumbukira ine, ndi kusaiwala mdzakazi wanu, mukapatsa mdzakazi wanu mwana wamwamuna, ine ndidzampereka kwa Yehova masiku onse a moyo wake, ndipo palibe lumo lidzapita pamutu pake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa