Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 25:16 - Buku Lopatulika

16 Cheukirani ine ndipo ndichitireni chifundo; pakuti ndili wounguluma ndi wozunzika.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Cheukirani ine ndipo ndichitireni chifundo; pakuti ndili wounguluma ndi wozunzika.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Inu Chauta yang'aneni ine, ndipo mundikomere mtima, pakuti ndili ndekhandekha, ndipo ndazunzika kwambiri.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Tembenukirani kwa ine ndipo mundikomere mtima, pakuti ndili ndekhandekha ndipo ndikuzunzika.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 25:16
12 Mawu Ofanana  

Pakuti ine ndine wozunzika ndi waumphawi, ndi mtima wanga walaswa m'kati mwanga.


Munditembenukire, ndi kundichitira chifundo, monga mumatero nao akukonda dzina lanu.


Potero mzimu wanga wakomoka mwa ine; mtima wanga utenga nkhawa m'kati mwanga.


Ndinavomera choipa changa kwa Inu; ndipo mphulupulu yanga sindinaibise. Ndinati, Ndidzaululira Yehova machimo anga; ndipo munakhululukira choipa cha kulakwa kwanga.


Mwatitaya Mulungu, mwatipasula; mwakwiya; tibwezereni.


Tcherani khutu lanu Yehova, mundiyankhe; pakuti ine ndine wozunzika ndi waumphawi.


Mundibwerere ine, ndi kundichitira chifundo; mpatseni mtumiki wanu mphamvu yanu, ndipo pulumutsani mwana wa mdzakazi wanu.


Ndipo tsopano, Mulungu wathu, mumvere pemphero la mtumiki wanu, ndi mapembedzero ake, nimuwalitse nkhope yanu pamalo anu opatulika amene ali opasuka, chifukwa cha Ambuye.


Adzabwera, nadzatichitira nsoni; adzagonjetsa mphulupulu zathu; ndipo mudzataya zochimwa zao zonse m'nyanja yakuya.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa