Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 18:49 - Buku Lopatulika

49 Chifukwa chake Yehova ndidzakuyamikani mwa amitundu, ndipo dzina lanu ndidzaliimbira.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

49 Chifukwa chake Yehova ndidzakuyamikani mwa amitundu, ndipo dzina lanu ndidzaliimbira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

49 Chifukwa cha zimenezi ndidzakutamandani Inu Chauta, pakati pa mitundu ya anthu, ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

49 Choncho ine ndidzakutamandani pakati pa anthu a mitundu ina, Inu Yehova; ndidzayimba nyimbo zotamanda dzina lanu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 18:49
11 Mawu Ofanana  

Wakhazikika mtima wanga, Mulungu; ndidzaimba, inde ndidzaimba zolemekeza, ndiko ulemerero wanga.


Ndidzakuyamikani mwa mitundu ya anthu, Yehova: ndipo ndidzaimba zakukulemekezani mwa anthu.


Mafumu onse a padziko lapansi adzakuyamikani, Yehova, popeza adamva mau a pakamwa panu.


Mwenzi chipulumutso cha Israele chitachokera ku Ziyoni! Pakubweretsa Yehova anthu ake a m'nsinga, pamenepo adzakondwera Yakobo, nadzasekera Israele.


kuti ulemu wanga uimbire Inu, wosakhala chete. Yehova Mulungu wanga, ndidzakuyamikani nthawi zonse.


Ndidzakuyamikirani mwa anthu, Ambuye, ndidzakuimbirani mwa mitundu.


Ndipo pamene anaimba nyimbo, anatuluka kunka kuphiri la Azitona.


ndi kuti anthu a mitundu ina akalemekeze Mulungu, chifukwa cha chifundo; monga kwalembedwa, Chifukwa cha ichi ndidzakuvomerezani Inu pakati pa anthu amitundu, ndidzaimbira dzina lanu.


Ndikulamulira pamaso pa Mulungu, wozipatsa zinthu zonse moyo, ndi Khristu Yesu, amene anachitira umboni chivomerezo chabwino kwa Pontio Pilato;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa