Masalimo 18:48 - Buku Lopatulika48 Andipulumutsa kwa adani anga. Inde mundikweza pa iwo akundiukira ine, mundikwatula kwa munthu wachiwawa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201448 Andipulumutsa kwa adani anga. Inde mundikweza pa iwo akundiukira ine, mundikwatula kwa munthu wachiwawa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa48 Ndiye amene adandipulumutsa kwa adani anga. Zoonadi Inu mudandikweza pamwamba pa ondiwukira, mudandilanditsa kwa anthu ankhanza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero48 amene amandipulumutsa mʼmanja mwa adani anga. Inu munandikuza kuposa adani anga; munandilanditsa mʼmanja mwa anthu ankhanza. Onani mutuwo |