Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 18:47 - Buku Lopatulika

47 Ndiye Mulungu amene andibwezerera chilango, nandigonjetsera mitundu ya anthu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

47 Ndiye Mulungu amene andibwezerera chilango, nandigonjetsera mitundu ya anthu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

47 Mulungu ndiye adandithandiza kuti ndilipsire, adagonjetsa anthu a mitundu ina, kuti akhale mu ulamuliro wanga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

47 Iye ndi Mulungu amene amabwezera chilango, amene amagonjetsa anthu a mitundu yonse amene ali pansi pa ulamuliro wanga,

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 18:47
7 Mawu Ofanana  

inde Mulungu wakundibwezera chilango ine, ndi kundigonjetsera anthu a mitundu.


Ndiye chifundo changa, ndi linga langa, msanje wanga, ndi Mpulumutsi wanga; chikopa changa, ndi Iye amene ndimtama; amene andigonjetsera anthu anga.


Atigonjetsera anthu, naika amitundu pansi pa mapazi athu.


Tiyeni tiimbire Yehova mokondwera; tifuule kwa thanthwe la chipulumutso chathu.


Yehova ndiye Mulungu wansanje, nabwezera chilango; Yehova ndiye wobwezera chilango, ndi waukali ndithu; Yehova ndiye wobwezera chilango oyambana naye, nasungira mkwiyo pa adani ake.


Musabwezere choipa, okondedwa, koma patukani pamkwiyo; pakuti kwalembedwa, Kubwezera kuli kwanga, Ine ndidzabwezera, ati Ambuye.


Kubwezera chilango nkwanga, kubwezera komwe, pa nyengo ya kuterereka phazi lao; pakuti tsiku la tsoka lao layandika, ndi zinthu zowakonzeratu zifulumira kudza.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa