Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 18:38 - Buku Lopatulika

38 Ndidzawapyoza kuti sangakhoze kuuka, adzagwa pansi pa mapazi anga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

38 Ndidzawapyoza kuti sangakhoze kuuka, adzagwa pansi pa mapazi anga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

38 Ndimaŵakantha koopsa kotero kuti sangathenso kudzuka, ndidaŵapondereza ndi mapazi anga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

38 Ndinakantha adaniwo kotero kuti sanathenso kudzuka; anagwera pa mapazi anga.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 18:38
13 Mawu Ofanana  

Ndinawatha ndi kuwapyoza, kuti sangathe kuuka, inde anagwa pansi pa mapazi anga.


Mudzawaika ngati ng'anjo yamoto pa nyengo ya mkwiyo wanu. Yehova adzawatha m'kukwiya kwake, ndipo moto udzawanyeketsa.


Pomwepo padagwera ochita zopanda pake. Anawalikha, ndipo sadzatha kuukanso.


Atigonjetsera anthu, naika amitundu pansi pa mapazi athu.


Yehova adzakantha adani anu akukuukirani; adzakudzerani njira imodzi, koma adzathawa pamaso panu njira zisanu ndi ziwiri.


Chomwecho Davide ndi anthu ake anamuka ku Keila, naponyana ndi Afilisti, natenga ng'ombe zao, nawapha ndi kuwapulula kwambiri. Motero Davide analanditsa okhala mu Keila.


Ndipo Davide anawakantha kuyambira madzulo kufikira usiku wa mawa wake; ndipo panalibe munthu mmodzi wa iwowa anapulumuka, koma anyamata mazana anai oberekeka pa ngamira, nathawa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa