Masalimo 18:37 - Buku Lopatulika37 Ndidzalondola adani anga, ndi kuwapeza, ndipo sindidzabwerera asanathe psiti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201437 Ndidzalondola adani anga, ndi kuwapeza, ndipo sindidzabwerera asanathe psiti. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa37 Ndidalondola adani anga ndi kuŵapeza, sindidabwerere mpaka nditaŵagonjetsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero37 Ndinathamangitsa adani anga ndi kuwapitirira; sindinabwerere mpaka atawonongedwa. Onani mutuwo |