Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 18:36 - Buku Lopatulika

36 Mwandipondetsa patalipatali, sanaterereke mapazi anga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

36 Mwandipondetsa patalipatali, sanaterereka mapazi anga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

36 Mudandikuzira njira yanga kuti ndiyendemo bwino, choncho mapazi anga sadaterereke.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

36 Munakulitsa njira yoyendamo ine, kuti mapazi anga asaguluke.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 18:36
9 Mawu Ofanana  

Munakulitsa kulunza kwanga pansi panga, ndi mapazi anga sanaterereke.


Mapondedwe ake amphamvu adzasautsidwa, ndi uphungu wakewake udzamgwetsa.


Inde akadakukopani muchoke posaukira, mulowe kuchitando kopanda chopsinja; ndipo zoikidwa pagome panu zikadakhala zonona ndithu.


Pakufuula ine mundiyankhe, Mulungu wa chilungamo changa; pondichepera mwandikulitsira malo. Ndichitireni chifundo, imvani pemphero langa.


Koma iwo amene afuna moyo wanga kuti auononge, adzalowa m'munsi mwake mwa dziko.


Mapazi ako sadzaombana ulikuyenda; ukathamanga, sudzaphunthwa.


usaope, pakuti Ine ndili pamodzi ndi iwe; usaopsedwe, pakuti Ine ndine Mulungu wako; ndidzakulimbitsa; inde, ndidzakuthangata; inde, ndidzakuchirikiza ndi dzanja langa lamanja la chilungamo.


Koma ndili ndi ubatizo ndikabatizidwe nao; ndipo ndikanikizidwa Ine kufikira ukatsirizidwa!


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa