Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 18:34 - Buku Lopatulika

34 Aphunzitsa manja anga agwire nkhondo; kuti walifuka uta wamkuwa ndi manja anga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

34 Aphunzitsa manja anga agwire nkhondo; kuti walifuka uta wamkuwa ndi manja anga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

34 Amaphunzitsa manja anga kamenyedwe ka nkhondo, kotero kuti ndingathe kupinda uta wachitsulo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

34 Iye amaphunzitsa manja anga kuchita nkhondo; manja anga amatha kuthyola uta wachitsulo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 18:34
8 Mawu Ofanana  

Ndiponso munandipatsa chikopa cha chipulumutso chanu; ndi kufatsa kwanu kunandikulitsa.


Wolemekezeka Yehova thanthwe langa, wakuphunzitsa manja anga achite nkhondo, zala zanga zigwirane nao:


Aletsa nkhondo ku malekezero a dziko lapansi; athyola uta, nadula nthungo; atentha magaleta ndi moto.


ndipo adzakhala mzimu wa chiweruziro kwa oweruza milandu, ndi mphamvu kwa iwo amene abweza nkhondo pachipata.


Atero Yehova kwa wodzozedwa wake kwa Kirusi, amene dzanja lake lamanja ndaligwiritsa, kuti agonjetse mitundu ya anthu pamaso pake, ndipo ndidzamasula m'chuuno mwa mafumu; atsegule zitseko pamaso pake, ndi zipata sizidzatsekedwa:


Yehova wa makamu atero: Taonani, ndidzathyola uta wa Elamu, ndiwo mtima wa mphamvu yao.


Ndipo kudzachitika tsiku lomwelo, ndidzathyola uta wa Israele m'chigwa cha Yezireele.


Yehova, Ambuye, ndiye mphamvu yanga, asanduliza mapazi anga ngati a mbawala, nadzandipondetsa pa misanje yanga.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa