Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 147:18 - Buku Lopatulika

18 Atumiza mau ake nazisungunula; aombetsa mphepo yake, ayenda madzi ake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Atumiza mau ake nazisungunula; aombetsa mphepo yake, ayenda madzi ake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Akalamula kuti zichoke, pomwepo zimasungunuka, akaombetsa mphepo, madzi amayenda.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Amatumiza mawu ake ndipo chisanucho chimasungunuka; amawombetsa mphepo ndipo madzi amayenda.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 147:18
7 Mawu Ofanana  

Mwa kupuma kwake Mulungu apereka chipale, ndi madzi achitando aundana.


Kodi mudziwa umo zovala zanu zifundira, pamene dziko lili thuu chifukwa cha mwera?


Atumiza mau ake nawachiritsa, nawapulumutsa ku chionongeko chao.


Atumiza lamulo lake kudziko lapansi; mau ake athamanga liwiro.


Pakuti ananena, ndipo chinachitidwa; analamulira, ndipo chinakhazikika.


Anaombetsa m'mwamba mphepo ya kum'mawa, natsogoza mwera ndi mphamvu yake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa