Masalimo 147:16 - Buku Lopatulika16 Apatsa chipale chofewa ngati ubweya; awaza chisanu ngati phulusa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Apatsa chipale chofewa ngati ubweya; awaza chisanu ngati phulusa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Amagwetsa chisanu chambee ngati ubweya. Amamwaza chipale ngati phulusa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Amagwetsa chisanu ngati ubweya ndi kumwaza chipale ngati phulusa. Onani mutuwo |