Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 147:12 - Buku Lopatulika

12 Yerusalemu, lemekezani Yehova; Ziyoni, lemekezani Mulungu wanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Yerusalemu, lemekezani Yehova; Ziyoni, lemekezani Mulungu wanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Tamanda Chauta, iwe Yerusalemu. Tamanda Mulungu wako, iwe Ziyoni.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Lemekeza Yehova, iwe Yerusalemu; tamanda Mulungu wako, iwe Ziyoni,

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 147:12
6 Mawu Ofanana  

Yehova adzachita ufumu kosatha, Mulungu wako, Ziyoni, ku mibadwomibadwo. Aleluya.


Akondwere Israele mwa Iye amene anamlenga; ana a Ziyoni asekere mwa mfumu yao.


Tafuula, takuwa iwe, wokhala mu Ziyoni, chifukwa Woyera wa Israele wa m'kati mwako ali wamkulu.


Ha, akongolatu pamapiri mapazi a iye amene adza ndi uthenga wabwino, amene abukitsa mtendere, amene adza ndi uthenga wabwino wa zinthu zabwino, amene abukitsa chipulumutso; amene ati kwa Ziyoni, Mulungu wako ndi mfumu.


Mukondwere tsono, inu ana a Ziyoni, nimusekerere mu Yehova Mulungu wanu; pakuti adzayamba kukupatsani mvula ya chizimalupsa, monga mwa chilungamo chake; nakuvumbitsirani mvula, mvula ya chizimalupsa ndi ya masika mwezi woyamba.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa