Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 145:7 - Buku Lopatulika

7 Adzabukitsa chikumbukiro cha ubwino wanu waukulu, nadzaimbira chilungamo chanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Adzabukitsa chikumbukiro cha ubwino wanu waukulu, nadzaimbira chilungamo chanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Adzasimba za ubwino wanu, adzaimba nyimbo zotamanda kulungama kwanu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Adzakondwerera kuchuluka kwa ubwino wanu, ndi kuyimba mwachimwemwe za chilungamo chanu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 145:7
16 Mawu Ofanana  

Tanimphitsani chifundo chanu pa iwo akudziwa Inu; ndi chilungamo chanu pa oongoka mtima.


Mundilanditse kumlandu wa mwazi, Mulungu, ndinu Mulungu wa chipulumutso changa; lilime langa lidzakweza nyimbo ya chilungamo chanu.


Chilungamo chanunso, Mulungu, chifikira kuthambo; Inu amene munachita zazikulu, akunga Inu ndani, Mulungu?


Akondwera m'dzina lanu tsiku lonse; ndipo akwezeka m'chilungamo chanu.


Ndidzatchula zachifundo chake cha Yehova, ndi matamando a Yehova, monga mwa zonse zimene Yehova wapereka kwa ife; ndi ubwino wake waukulu kwa banja la Israele, umene Iye wapereka kwa iwo, monga mwa chifundo chake, ndi monga mwa ntchito zochuluka za chikondi chake.


Masiku ake Yuda adzapulumutsidwa, ndipo Israele adzakhala mokhazikika, dzina lake adzatchedwa nalo, ndilo Yehova ndiye chilungamo chathu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa