Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 145:5 - Buku Lopatulika

5 Ndidzalingalira ulemerero waukulu wa ulemu wanu, ndi ntchito zanu zodabwitsa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ndidzalingalira ulemerero waukulu wa ulemu wanu, ndi ntchito zanu zodabwitsa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Ndidzasinkhasinkha za ulemerero ndi za ufumu wanu waukulu, ndidzalingalira za ntchito zanu zodabwitsa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Adzayankhula ulemerero wokongola waufumu wanu, ndipo ine ndidzalingalira za ntchito zanu zodabwitsa.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 145:5
16 Mawu Ofanana  

Ndipo Isaki anatuluka kulingalira m'munda madzulo; ndipo anatukula maso ake, nayang'ana, taona, ngamira zinalinkudza.


Muimbireni, muimbireni zomlemekeza; fotokozerani zodabwitsa zake zonse.


Muimbireni, muimbireni zomlemekeza; fotokozerani zodabwitsa zake zonse.


Chochita Iye ncha ulemu, ndi ukulu: Ndi chilungamo chake chikhalitsa kosatha.


Mundizindikiritse njira ya malangizo anu; kuti ndilingalire zodabwitsa zanu.


Lilime langa lomwe lidzalankhula za chilungamo chanu tsiku lonse, pakuti ofuna kundichitira choipa achita manyazi, nadodoma.


Wolemekezeka Yehova Mulungu, Mulungu wa Israele, amene achita zodabwitsa yekhayo.


Fotokozerani ulemerero wake mwa amitundu; zodabwitsa zake mwa mitundu yonse ya anthu.


Tsiku lomwelo mudzati, Muyamikire Yehova, bukitsani dzina lake, mulalikire machitidwe ake mwa mitundu ya anthu, munene kuti dzina lake lakwezedwa.


Tsono ine Nebukadinezara ndiyamika, ndi kukuza, ndi kulemekeza Mfumu ya Kumwamba, pakuti ntchito zake zonse nzoona, ndi njira zake chiweruzo; ndi oyenda m'kudzikuza kwao, Iye akhoza kuwachepetsa.


Pakuti ndidzalalika dzina la Yehova. Nenani kuti Mulungu wathu ndi wamkulu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa