Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 145:16 - Buku Lopatulika

16 Muolowetsa dzanja lanu, nimukwaniritsira zamoyo zonse chokhumba chao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Muolowetsa dzanja lanu, nimukwaniritsira zamoyo zonse chokhumba chao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Mumafumbatula dzanja lanu, ndipo mumapatsa chamoyo chilichonse zofuna zake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Mumatsekula dzanja lanu ndi kukwaniritsa zokhumba za chamoyo chilichonse.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 145:16
6 Mawu Ofanana  

Ndipo iwe udzitengereko wekha zakudya zonse zodyedwa, nudzisonkhanitsire izi wekha: ndipo zidzakhala zakudya za iwe ndi za iwo.


kukhutitsa thengo la kunkhwangwala, ndi kuphukitsa msipu?


Chimene muzipatsa zigwira; mufumbatula dzanja lanu, zikhuta zabwino.


Pakuti akhutitsa mtima wolakalaka, nadzaza mtima wanjala ndi zabwino.


Ndidzadalitsatu chakudya chake; aumphawi ake ndidzawakhutitsa ndi mkate.


Amene apatsa zoweta chakudya chao, ana a khwangwala alikulira.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa