Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 145:12 - Buku Lopatulika

12 Kudziwitsa ana a anthu zamphamvu zake, ndi ulemerero waukulu wa ufumu wake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Kudziwitsa ana a anthu zamphamvu zake, ndi ulemerero waukulu wa ufumu wake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 kuti adziŵitse anthu onse za ntchito zanu zamphamvu, kutinso asimbe za ulemerero ndi za ufumu wanu waukulu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 kuti anthu onse adziwe za machitidwe anu amphamvu ndi ulemerero wokongola wa ufumu wanu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 145:12
15 Mawu Ofanana  

Yamikani Yehova, itanirani pa dzina lake; bukitsani mwa mitundu ya anthu zochita Iye.


Kumbukirani zodabwitsa zake adazichita; zizindikiro zake ndi maweruzo a pakamwa pake;


Adzafotokoza ndani ntchito zamphamvu za Yehova, adzamveketsa ndani chilemekezo chake chonse?


Anaonetsera anthu ake mphamvu ya ntchito zake, pakuwapatsa cholowa cha amitundu.


Muimbireni Yehova nyimbo yatsopano; popeza anachita zodabwitsa: Dzanja lake lamanja, mkono wake woyera, zinamchitira chipulumutso.


Ndipo Yesu anadza nalankhula nao, nanena, Mphamvu zonse zapatsidwa kwa Ine Kumwamba ndi padziko lapansi.


Ndipo ndinamva mau aakulu mu Mwamba, nanena, Tsopano zafika chipulumutso, ndi mphamvu, ndi ufumu za Mulungu wathu, ndi ulamuliro wa Khristu wake; pakuti wagwetsedwa wonenera wa abale athu, wakuwanenera pamaso pa Mulungu wathu usana ndi usiku.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa