Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 145:11 - Buku Lopatulika

11 Adzanenera ulemerero wa ufumu wanu, adzalankhulira mphamvu yanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Adzanenera ulemerero wa ufumu wanu, adzalankhulira mphamvu yanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Adzalankhula za ulemerero wa ufumu wanu, adzasimba za mphamvu zanu,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Iwo adzafotokoza za ulemerero wa ufumu wanu ndi kuyankhula za mphamvu yanu,

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 145:11
18 Mawu Ofanana  

Nenani mwa amitundu, Yehova achita ufumu; dziko lokhalamo anthu lomwe likhazikika kuti silingagwedezeke; adzaweruza mitundu ya anthu molunjika.


Ndipo padzatuluka mphukira pa tsinde la Yese, ndi nthambi yotuluka m'mizu yake idzabala zipatso;


Ndipo padzakhala tsiku lomwelo, kuti muzu wa Yese umene uima ngati mbendera ya mitundu ya anthu, amitundu adzafunafuna uwu; ndipo popuma pake padzakhala ulemerero.


Pompo mwezi udzanyazitsidwa, ndi dzuwa lidzakhala ndi manyazi, pakuti Yehova wa makamu adzalamulira chaulemerero m'phiri la Ziyoni, ndi mu Yerusalemu, ndi pamaso pa akuluakulu ake.


Kondwera kwambiri, mwana wamkazi wa Ziyoni; fuula mwana wamkazi wa Yerusalemu; taona, Mfumu yako ikudza kwa iwe; ndiye wolungama, ndi mwini chipulumutso; wofatsa ndi wokwera pabulu, ndi mwana wamphongo wa bulu.


Ndipo musatitengere kokatiyesa, koma mutipulumutse kwa woipayo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa