Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 144:7 - Buku Lopatulika

7 Tulutsani manja anu kuchokera m'mwamba; ndikwatuleni ndi kundilanditsa kumadzi aakulu, kudzanja la alendo;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Tulutsani manja anu kuchokera m'mwamba; ndikwatuleni ndi kundilanditsa kumadzi aakulu, kudzanja la alendo;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Tambasulani dzanja lanu kuchokera kumwamba. Landitseni ndi kundipulumutsa ku madzi ozama, omboleni m'manja mwa akunja,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Tambasulani dzanja lanu kuchokera kumwamba; landitseni ndi kundipulumutsa, ku madzi amphamvu, mʼmanja mwa anthu achilendo,

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 144:7
15 Mawu Ofanana  

Iye anatumiza kuchokera kumwamba nanditenga; Iye ananditulutsa m'madzi aakulu.


Nadzipatula a mbumba ya Israele kwa alendo onse, naimirira, nawulula zochimwa zao, ndi mphulupulu za makolo ao.


Akadatimiza madziwo, mtsinje ukadapita pa moyo wathu;


Ndilanditseni ndi kundipulumutsa kudzanja la alendo, amene pakamwa pao alankhula zachabe, ndi dzanja lao lamanja ndilo dzanja lachinyengo.


Anatuma kuchokera m'mwamba, ananditenga; anandivuula m'madzi ambiri.


Anandipulumutsa ine kwa mdani wanga wamphamvu, ndi kwa iwo ondida ine, pakuti anandiposa mphamvu.


Pakumva m'khutu za ine adzandimvera, alendo adzandigonjera monyenga.


Pakuti alendo andiukira, ndipo oopsa afunafuna moyo wanga; sadziikira Mulungu pamaso pao.


Yuda wachita monyenga, ndi mu Israele ndi mu Yerusalemu mwachitika chonyansa; pakuti Yuda waipsa chipatuliko cha Yehova chimene achikonda, nakwatira mwana wamkazi wa mulungu wachilendo.


Amakhulupirira Mulungu; Iye ampulumutse tsopano, ngati amfuna; pakuti anati, Ine ndine Mwana wa Mulungu.


Ndipo anena ndi ine, Madziwo udawaona uko akhalako mkazi wachigololoyo ndiwo anthu, ndi makamu, ndi mitundu, ndi manenedwe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa