Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 144:6 - Buku Lopatulika

6 Ng'animitsani mphezi, ndi kuwabalalitsa; tumizani mivi yanu, ndi kuwapirikitsa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Ng'animitsani mphezi, ndi kuwabalalitsa; tumizani mivi yanu, ndi kuwapirikitsa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Ng'animitsani zing'aning'ani ndi kuŵamwaza adani anga. Ponyani mivi yanu, ndi kuŵapirikitsa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Tumizani zingʼaningʼani ndi kubalalitsa adani; ponyani mivi yanu ndi kuwathamangitsa.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 144:6
10 Mawu Ofanana  

Ndipo zidaoneka zoyendamo madzi, nafukuka maziko a dziko lapansi, mwa kudzudzula kwanu, Yehova, mwa mpumo wa mpweya wa m'mphuno mwanu.


Pakuti mudzawabweza m'mbuyo, popiringidza m'nsinga zanu pankhope pao.


Mivi yanu njakuthwa; mitundu ya anthu igwa pansi pa inu; iwalasa mumtima adani a mfumu.


Adzawakhumudwitsa, lilime lao lidzawatsutsa; onse akuwaona adzawathawa.


Ndidzawaunjikira zoipa; ndidzawathera mivi yanga.


Mivi yanga ndiiledzeretsa nao mwazi, ndi lupanga langa lidzalusira nyama; ndi mwazi wa ophedwa ndi ogwidwa, ndi mutu wachitsitsi wa mdani.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa