Masalimo 144:5 - Buku Lopatulika5 Weramutsani thambo lanu, Yehova, nimutsike: Khudzani mapiri ndipo adzafuka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Weramutsani thambo lanu, Yehova, nimutsike: Khudzani mapiri ndipo adzafuka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Ng'ambani thambo, Inu Chauta, ndi kutsikira pansi. Khudzani mapiri kuti afuke nthunzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Ngʼambani mayiko akumwamba, Inu Yehova, ndipo tsikani pansi; khudzani mapiri kuti atulutse utsi. Onani mutuwo |