Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 144:10 - Buku Lopatulika

10 Ndiye amene apatsa mafumu chipulumutso: Amene alanditsa Davide mtumiki wake kulupanga loipa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Ndiye amene apatsa mafumu chipulumutso: Amene alanditsa Davide mtumiki wake kulupanga loipa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Inu amene mumapambanitsa mafumu pankhondo, amene mumalanditsa Davide mtumiki wanu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 kwa Iye amene amapambanitsa mafumu, amene amapulumutsa Davide mtumiki wake ku lupanga loopsa.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 144:10
12 Mawu Ofanana  

Ndipo Naamani kazembe wa khamu la nkhondo la mfumu ya Aramu anali munthu womveka pamaso pa mbuyake, ndi waulemu; popeza mwa iye Yehova adapulumutsa Aaramu; ndiyenso ngwazi, koma wakhate.


Chifukwa cha Davide mtumiki wanu musabweze nkhope ya wodzozedwa wanu.


Yehova Ambuye, ndinu mphamvu ya chipulumutso changa, munandiphimba mutu wanga tsiku lakulimbana nkhondo.


Yehova, musampatse woipa zokhumba iye; musamthandize zodzipanga zake; angadzikuze.


Alanditsa mfumu yake ndi chipulumutso chachikulu; nachitira chifundo wodzozedwa wake, Davide, ndi mbumba yake, kunthawi zonse.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa